[Verse]
A Phiri anabwela kuchoka ku Harare eeh
A Phiri anabwela kuchoka ku Harare eeh
Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse anamwalira ku Dara
A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse anamwalira ku Dara

[Pre-Chorus]
Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse Anamwalira ku Dara
Anamwalira ku Dara
Oh, sitigawana

[Chorus]
Oh, sitigawana
Sitigawana
Oh, sitigawana zida
Umandikondera M'mene umandikondera Ife
Sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana zida
Sitigawana
Ife sitigawana, sitigawana
Oh, sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana
Oh, sitigawana zida
Umandikondera
M'mene umandikondera
Ife sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana
Oh, sitigawana zida
Umandikondera M'mene umandikondera
Anamwalira ku Dara
Comments (0)
The minimum comment length is 50 characters.
Information
There are no comments yet. You can be the first!
Login Register
Log into your account
And gain new opportunities
Forgot your password?